Kudziwa Zambiri za eGame Solution

eGame Solution (ndi nthambi ya guru la M. POS), tili ndi ukadauro wodziwa bwino kupeleka njira zabwino zamakono zogwiritsira tchito makina, tilinso ndi guru loyendetsa ntchito la anthu la luso, zinthu zathu zomwe tikupanga ndi zopangidwa bwino, timapelekanso njira zogwiritsira tchito makina za makono zomwe zikugwiritsidwa tchito mzaka zino, komanso njira zabwino zotukura masewelo apamagetsi. Timakonza njira zabwino kwa ogura athu kuti athe ku kwanilitsa zofuna zakumtima kwao.

Momwe Takhara Tikuchitira

Mfundo zathu zogwilira tchito zinapatsidwa chilorezo chogwiritsa ntchito ISO/IEC 27001:2013, imene ili ndondomeko yabwino yofunikira popanga mfundo kuti zizitha kukhara zotetezeka bwino.
ISO 27001 ndi njira yapaderadera yothandiza kusunga bwino mfundo (ISMS). Njira yothandizira kusunga mfundo imeneyi ndi yomwe imathandiza kukhara ngati ngodya ya ndondomeko zomwe zimakhazikitsidwa pa Bungwe komanso machitidwe a zinthu, ku phatikizapo zonse za malamulo, njira zothandizira za makina ngakhalenso nzeru za anthu zomwe zimathandiza kusunga bwino mfundo.


Yankho la Zinthu Zapamwamba Zomwe Timapanga ku eGAME

M. Lottery ndi dzina lamalonda la masewero athu apamagetsi omwe angathe kulumikizidwa ndi njira zina zambiri za lotale zopelekedwa ndi a eGame kapena njira zina za athu ena apadera, zomwe zikubweretsa magwiritsidwe tchito abwino komanso wodalirika pa masewero apamagetsi ndi a lotale. Masewero apamagetsi monga Loto (6/36,6/49,5/90/ etc),sport Totalizator,sports Betting, Istant Game, Bingo, Keno, Chance(Lotale yowelengetsera) onse amathandizidwira pamodzi.


Mbali Yathu ya Ukadaulo

Cholinga cha eGames ndikupereka magwiritsidwe tchito abwino apamwamba a makina, ndikutha ku yang'anira bwino oyendetsa onse mumayiko osiyanasiyana, ndicholinga chakuti athe kuchepetsa zovuta zomwe zimatha kubwera pa malonda komano kuti athe kuwonjezera phindu lawo.

  • Lotale ya mmagetsi, Masewera a mmagetsi, kupanga ndondomeko za betchi
  • Kukhazikitsa ndondomeko za lotale,ndi mayankho a turnkey
  • Kuthandiza kukonza dongosolo
  • Kudziwa mokuya za mayendetsedwe ndi machitidwe
  • Kukonza mbiri ya zomwe mumapanga
  • Njira zopangira malonda
  • Kupanga masewera atsopano
  • Kuwonjezera chikoka,kutukura ndiku lengezera
  • Zinthu zongochitika ndi makonzedwe a zinthu zikavuta
  • BOT (Kumanga-kugwira ntchito- kutumiza)


Maso Mphenya Athu

A eGame Timafunitsitsa kukhara oyambilira kupereka mayankho komanso njira ndi mwayi ku gawo la masewelo obetcha ndi a lotale, kwinaku tikuwapangira osewera zowasangalatsa zambiri ndi kuwatukura umoyo wawo.

Ngati mukufuna kudziwa zambiri za zinthu zomwe tili nazo, chonde lumikizanani nafe pa:

eGame Solutions
Unit 212, Photonics Centre,
Hong Kong Science Park, Hong Kong
tel: +852 2388 8112
faks: +852 2388 8661
Email: info@egame-solutions.com
Website: www.egame-solutions.com